Yobu 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndithu udzaona kuti ana ako ndi ambiri,+Ndipo mbadwa zako zidzakhala ngati zomera za padziko lapansi.+
25 Ndithu udzaona kuti ana ako ndi ambiri,+Ndipo mbadwa zako zidzakhala ngati zomera za padziko lapansi.+