Yobu 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Udzakhala ndi mphamvube mpaka kulowa m’manda,+Mofanana ndi ngala zokhwima za tirigu, zimene amazisanjikiza pamodzi pamalo opunthira tirigu pa nyengo yake.
26 Udzakhala ndi mphamvube mpaka kulowa m’manda,+Mofanana ndi ngala zokhwima za tirigu, zimene amazisanjikiza pamodzi pamalo opunthira tirigu pa nyengo yake.