Yobu 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mnofu wanga wakutidwa ndi mphutsi+ ndipo wamatirira fumbi,+Khungu langa lang’ambika n’kumatuluka mafinya.+
5 Mnofu wanga wakutidwa ndi mphutsi+ ndipo wamatirira fumbi,+Khungu langa lang’ambika n’kumatuluka mafinya.+