Yobu 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye amawadziwa bwino amuna onyenga.+Akaona zoipa zikuchitidwa, kodi sadzakhudzidwa nazo?