Yobu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu angauze anzake kuti atengepo mbali yawo,Koma maso a ana ake adzachita mdima.+