Yobu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mpweya wanga wasanduka wonyansa kwa mkazi wanga,+Ndipo ndakhala wonunkha kwa ana obadwa kwa mayi anga.
17 Mpweya wanga wasanduka wonyansa kwa mkazi wanga,+Ndipo ndakhala wonunkha kwa ana obadwa kwa mayi anga.