Yobu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kwa iye zibuma za dothi lochokera m’chigwa* zidzakhala zotsekemera.+Pambuyo pake adzakoka anthu onse,+Ndipo amene anapita iye asanapite n’ngosawerengeka.
33 Kwa iye zibuma za dothi lochokera m’chigwa* zidzakhala zotsekemera.+Pambuyo pake adzakoka anthu onse,+Ndipo amene anapita iye asanapite n’ngosawerengeka.