Yobu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso amene amauza Mulungu woona kuti: ‘Tichokereni!+Kodi Wamphamvuyonse angatichite chiyani?’