Yobu 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako udzasangalala kwambiri ndi Wamphamvuyonse,+Ndipo udzakweza nkhope yako kwa Mulungu.+