Yobu 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zimene waganiza kuti uchite zidzatheka,Ndipo kuwala kudzaunikira njira zako.+