Yobu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “N’chifukwa chiyani Wamphamvuyonse sanakhazikitse nthawi yachiweruzo,+Ndipo n’chifukwa chiyani omudziwa sanaone masiku ake achiweruzo?+
24 “N’chifukwa chiyani Wamphamvuyonse sanakhazikitse nthawi yachiweruzo,+Ndipo n’chifukwa chiyani omudziwa sanaone masiku ake achiweruzo?+