Yobu 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amapatutsa osauka panjira,+Ndipo pa nthawi yomweyo ozunzika a padziko lapansi amakhala atabisala.