-
Yobu 24:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 M’munda wa munthu wina, osauka amakololamo chakudya cha ziweto,
Ndipo iwo amalanda msangamsanga zinthu za m’munda wa mpesa wa munthu woipa.
-