Yobu 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Woipa amachita zoipa ndi mkazi wouma amene sabereka,Komanso ndi mkazi wamasiye+ amene woipayo sam’chitira zabwino.
21 Woipa amachita zoipa ndi mkazi wouma amene sabereka,Komanso ndi mkazi wamasiye+ amene woipayo sam’chitira zabwino.