Yobu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako n’kutha.+Iwo amatsitsidwa,+ ndipo mofanana ndi wina aliyense amathotholedwa.Amadulidwa mofanana ndi nsonga ya ngala za tirigu.
24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako n’kutha.+Iwo amatsitsidwa,+ ndipo mofanana ndi wina aliyense amathotholedwa.Amadulidwa mofanana ndi nsonga ya ngala za tirigu.