Yobu 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ulamuliro ndi wake ndipo iye ndi wochititsa mantha.+Iye amakhazikitsa mtendere kumwamba.