Yobu 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akamumvera ndi kumutumikira,Adzamaliza bwino masiku awo,Ndipo adzamaliza zaka zawo mosangalala.+