Yobu 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzafa ali anyamata,+Ndipo moyo wawo udzathera pakati pa mahule aamuna a pakachisi.+