Yobu 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndithu iye adzakukopani n’kukuchotsani pakamwa pa zowawa.+M’malomwake padzakhala malo otakasuka,+ osati opanikiza,Ndipo chitonthozo cha patebulo panu chidzakhala chodzaza ndi mafuta.+
16 Ndithu iye adzakukopani n’kukuchotsani pakamwa pa zowawa.+M’malomwake padzakhala malo otakasuka,+ osati opanikiza,Ndipo chitonthozo cha patebulo panu chidzakhala chodzaza ndi mafuta.+