Yobu 36:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndani wam’funsa kuti afotokoze za njira yake,+Ndipo ndani wamuuza kuti, ‘Mwachita zosalungama’?+