Yobu 36:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Amaikuta ndi kuwala kwake,+Ndipo waphimba mizu ya nyanja.