Salimo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.
12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.