Salimo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+Pakuti Yehova ali pakati pa khamu* la anthu olungama.+