Salimo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova, pulumutsani mfumu!+Tsiku limene tidzaitana, Mulungu adzatiyankha.+