Salimo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anditsegulira pakamwa pawo mondiopseza,+Ngati mkango wokhadzula nyama umenenso ukubangula.+