Salimo 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pitirizani kusonyeza kukoma mtima kwanu kosatha kwa anthu okudziwani,+Ndiponso chilungamo chanu kwa anthu owongoka mtima.+
10 Pitirizani kusonyeza kukoma mtima kwanu kosatha kwa anthu okudziwani,+Ndiponso chilungamo chanu kwa anthu owongoka mtima.+