Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+
12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+