Salimo 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:7 Galamukani!,9/2009, tsa. 28
7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+