Salimo 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi thandizo lanu tidzakankha adani athu.+M’dzina lanu tidzapondereza amene akutiukira.+