Salimo 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:17 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 12
17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.