Salimo 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ombani m’manja anthu nonsenu.+Fuulirani Mulungu mokondwera chifukwa chakuti wapambana.+