Salimo 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:20 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 9
20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+