Salimo 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Asungunuke ndi kupita ngati madzi.+Mulungu akunge uta woponyera mivi yake pamene adaniwo akugwa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:7 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 10