Salimo 59:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Madzulo amabweranso.+Ndipo amauwa ngati agalu+ ndi kuzungulira mzinda wonse.+