Salimo 61:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti inu mwakhala pothawirapo panga,+Nsanja yolimba pamaso pa mdani.+