Salimo 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+
6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+