Salimo 67:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu adzatidalitsa,+Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa.+