Salimo 72:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 72:16 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 3210/15/1986, tsa. 31
16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+