Salimo 77:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 77:6 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 12
6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama.