Salimo 77:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Madzi akuonani, inu Mulungu,Madzi akuonani, ndipo ayamba kumva ululu woopsa.+Komanso madzi akuya ayamba kuwinduka.+
16 Madzi akuonani, inu Mulungu,Madzi akuonani, ndipo ayamba kumva ululu woopsa.+Komanso madzi akuya ayamba kuwinduka.+