Salimo 81:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikanagonjetsa adani awo mosavuta,+Ndipo ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+