Salimo 82:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithudi, mudzafa mmene anthu onse amafera.+Ndipo mudzagwa mmene kalonga aliyense amagwera!’”+