Salimo 83:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amakumana mwachinsinsi kuti akambirane zochitira chiwembu anthu anu.+Ndipo amakonzera chiwembu anthu anu obisika.+
3 Iwo amakumana mwachinsinsi kuti akambirane zochitira chiwembu anthu anu.+Ndipo amakonzera chiwembu anthu anu obisika.+