Salimo 83:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+
11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+