Salimo 84:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 84:2 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, tsa. 8
2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+