Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:13 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, ptsa. 16-17
13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+