Salimo 88:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwandiika m’dzenje lakuya kwambiri,M’malo a mdima, m’phompho lalikulu.+