Salimo 89:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi imeneyo munalankhula ndi okhulupirika anu mwa masomphenya,+Ndipo munati:“Ndapereka thandizo kwa wamphamvu.+Ndakweza wosankhidwa mwapadera pakati pa anthu.+
19 Pa nthawi imeneyo munalankhula ndi okhulupirika anu mwa masomphenya,+Ndipo munati:“Ndapereka thandizo kwa wamphamvu.+Ndakweza wosankhidwa mwapadera pakati pa anthu.+