Salimo 89:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kukhulupirika kwanga ndi kukoma mtima kwanga kosatha kuli pa iye,+Ndipo nyanga yake imakwezedwa m’dzina langa.+
24 Kukhulupirika kwanga ndi kukoma mtima kwanga kosatha kuli pa iye,+Ndipo nyanga yake imakwezedwa m’dzina langa.+