Salimo 89:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kodi zochita zanu zakale zija zosonyeza kukoma mtima kosatha zili kuti, inu Yehova?Zija zimene munalumbira kwa Davide chifukwa cha kukhulupirika kwanu?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 89:49 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, tsa. 30
49 Kodi zochita zanu zakale zija zosonyeza kukoma mtima kosatha zili kuti, inu Yehova?Zija zimene munalumbira kwa Davide chifukwa cha kukhulupirika kwanu?+